Chimwemwe Chosatha
Video
Other languages
Share text
Share link
Show times
Hide times
00:00:14
M’mwamba mwadzaza nyenyezi
Zikuwalatu.00:00:21
00:00:21
Masananso Kukongola
M’matikondadi.00:00:28
00:00:28
M’nalenga nyanja ndi mtunda, ndi zonse timaonazi
Munamva bwino.00:00:39
00:00:42
Tonse tikusangalala,
N’za chipulumutso chathu,
Ndi dziko latsopano.00:00:54
00:00:55
Kukondedwa ndi ’nu M’lungu
Ndi mwayidi wapadera.
Ndinutu m’matipatsa00:01:08
00:01:09
Chimwemwe chosatha.00:01:15
00:01:31
Tili n’zonse zofunika
Zosangalatsa00:01:38
00:01:38
Munatilenga mwaluso,
Timamva bwino.00:01:45
00:01:45
Munatipatsatu mtima, wofuna kukhala moyo
Mpakatu kale.00:01:56
00:01:59
Tonse tikusangalala,
N’za chipulumutso chathu,
Ndi dziko latsopano.00:02:11
00:02:13
Kukondedwa ndi ’nu M’lungu
Ndi mwayidi wapadera.
Ndinutu m’matipatsa00:02:26
00:02:27
Chimwemwe chosatha.00:02:32
00:02:42
Popandatu Yesu
Chimwemwe panalibe.00:02:48
00:02:49
Iyetu anatifera
Ndiye chimwemwe n’chosatha.00:02:58
00:02:59
Tonse tikusangalala,
N’za chipulumutso chathu,
Ndi dziko latsopano.00:03:11
00:03:13
Kukondedwa ndi ’nu M’lungu
Ndi mwayidi wapadera.
Ndinutu m’matipatsa00:03:25
00:03:26
Chimwemwe chosatha.00:03:32
00:03:33
Tonse tikusangalala,
N’za chipulumutso chathu,
Ndi dziko latsopano.00:03:46
00:03:47
Kukondedwa ndi ’nu M’lungu
Ndi mwayidi wapadera.
Ndinutu m’matipatsa00:04:00
00:04:01
Chimwemwe chosatha.00:04:07
Chimwemwe Chosatha
-
Chimwemwe Chosatha
M’mwamba mwadzaza nyenyezi
Zikuwalatu.
Masananso Kukongola
M’matikondadi.
M’nalenga nyanja ndi mtunda, ndi zonse timaonazi
Munamva bwino.
Tonse tikusangalala,
N’za chipulumutso chathu,
Ndi dziko latsopano.
Kukondedwa ndi ’nu M’lungu
Ndi mwayidi wapadera.
Ndinutu m’matipatsa
Chimwemwe chosatha.
Tili n’zonse zofunika
Zosangalatsa
Munatilenga mwaluso,
Timamva bwino.
Munatipatsatu mtima, wofuna kukhala moyo
Mpakatu kale.
Tonse tikusangalala,
N’za chipulumutso chathu,
Ndi dziko latsopano.
Kukondedwa ndi ’nu M’lungu
Ndi mwayidi wapadera.
Ndinutu m’matipatsa
Chimwemwe chosatha.
Popandatu Yesu
Chimwemwe panalibe.
Iyetu anatifera
Ndiye chimwemwe n’chosatha.
Tonse tikusangalala,
N’za chipulumutso chathu,
Ndi dziko latsopano.
Kukondedwa ndi ’nu M’lungu
Ndi mwayidi wapadera.
Ndinutu m’matipatsa
Chimwemwe chosatha.
Tonse tikusangalala,
N’za chipulumutso chathu,
Ndi dziko latsopano.
Kukondedwa ndi ’nu M’lungu
Ndi mwayidi wapadera.
Ndinutu m’matipatsa
Chimwemwe chosatha.
-