JW subtitle extractor

Ndi Maso a Chikhulupiriro

Video Other languages Share text Share link Show times

Ndioperenji mkango?
Ndioperenji anthu?
Yehovatu alipo ndiopenso chani!
M’lungu andipulumutsa.
Ndi masotu a chikhulupiriro
Sindidzaopa chilichonsecho.
Yehovatu alipo sindichita mantha,
Amakhala nane pafupi
An’thandiza.
Atumiki akale
Anakhulupirika.
Chikhulupiriro chinawathandiza.
M’lungu adzawaukitsa.
Ndi masotu a chikhulupiriro
Sindidzaopa chilichonsecho.
Yehovatu alipo sindichita mantha,
Amakhala nane pafupi
An’thandiza.
Ndi Yehova, zonse ndi zotheka
Ndili n’chikhulupiriro.
Chikhulupiriro chathandiza kuti
Ndipirire pa mavuto.
M’lungu wandilonjeza
Tsogolo labwino.
Ndipirirebe
Poti posachedwa Yehova athetsa mavuto.
Ndi masotu a chikhulupiriro
Sindidzaopa chilichonsecho.
Yehovatu alipo sindichita mantha,
Amakhala nane pafupi
An’thandiza.
An’thandiza.